Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+ Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu. Miyambo 6:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.Zilipo zinthu 7 zimene amanyansidwa nazo: 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja amene amakhetsa magazi a anthu osalakwa,+ 1 Petulo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu “amene amakonda moyo wake komanso amafuna kumakhala moyo wabwino, ayenera kusamala kuti asamalankhule zoipa ndi lilime lake+ ndiponso kuti asamalankhule zachinyengo ndi milomo yake.
6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu.
16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.Zilipo zinthu 7 zimene amanyansidwa nazo: 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja amene amakhetsa magazi a anthu osalakwa,+ 1 Petulo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu “amene amakonda moyo wake komanso amafuna kumakhala moyo wabwino, ayenera kusamala kuti asamalankhule zoipa ndi lilime lake+ ndiponso kuti asamalankhule zachinyengo ndi milomo yake.
10 Munthu “amene amakonda moyo wake komanso amafuna kumakhala moyo wabwino, ayenera kusamala kuti asamalankhule zoipa ndi lilime lake+ ndiponso kuti asamalankhule zachinyengo ndi milomo yake.