1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amateteza mapazi a okhulupirika ake,+Koma anthu oipa adzawakhalitsa chete mumdima,+Popeza munthu sapambana chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 145:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amayangʼanira onse amene amamukonda,+Koma oipa onse adzawawononga.+
9 Amateteza mapazi a okhulupirika ake,+Koma anthu oipa adzawakhalitsa chete mumdima,+Popeza munthu sapambana chifukwa cha mphamvu zake.+