Yesaya 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti: “Limbani mtima. Musachite mantha. Chifukwa Mulungu wanu adzabwera nʼkudzabwezera adani anu.Mulungu adzabwera kudzapereka chilango.+ Iye adzabwera ndipo adzakupulumutsani.”+
4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti: “Limbani mtima. Musachite mantha. Chifukwa Mulungu wanu adzabwera nʼkudzabwezera adani anu.Mulungu adzabwera kudzapereka chilango.+ Iye adzabwera ndipo adzakupulumutsani.”+