Salimo 65:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ 3 Zolakwa zanga zandikulira,+Koma inu mumatikhululukira machimo athu.+
2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ 3 Zolakwa zanga zandikulira,+Koma inu mumatikhululukira machimo athu.+