Yakobo 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati munthu akuganiza kuti amalambira Mulungu,* koma satha kulamulira lilime lake,+ akudzipusitsa* ndipo kulambira kwake nʼkopanda phindu. Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma palibe munthu amene angathe kuweta lilime. Lilime ndi losalamulirika ndipo limavulaza komanso ndi lodzaza ndi poizoni wakupha.+
26 Ngati munthu akuganiza kuti amalambira Mulungu,* koma satha kulamulira lilime lake,+ akudzipusitsa* ndipo kulambira kwake nʼkopanda phindu.
8 Koma palibe munthu amene angathe kuweta lilime. Lilime ndi losalamulirika ndipo limavulaza komanso ndi lodzaza ndi poizoni wakupha.+