-
Deuteronomo 29:19, 20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma ngati wina wamva mawu a lumbiro ili nʼkulankhula modzitama mumtima mwake kuti, ‘Ndikhala ndi mtendere ngakhale kuti ndikuyendabe motsatira zofuna za mtima wanga,’ zimene zidzachititse kuti aliyense woyandikana naye* awonongedwe, 20 Yehova sadzafuna kukhululukira munthu woteroyo.+ Mʼmalomwake, mkwiyo waukulu wa Yehova udzamuyakira, ndipo matemberero onse amene alembedwa mʼbuku ili adzamugwera,+ ndipo Yehova adzachotseratu dzina la munthuyo pansi pa thambo.
-