Yesaya 45:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa Yehova,Mlengi wakumwamba,+ Mulungu woona,Amene anaumba dziko lapansi, amene analipanga ndi kulikhazikitsa mwamphamvu,+Amene sanalilenge popanda cholinga,* koma analiumba kuti anthu akhalemo,+ wanena kuti: “Ine ndine Yehova ndipo palibenso wina. Mateyu 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Osangalala ndi anthu ofatsa+ chifukwa adzalandira dziko lapansi.+ Chivumbulutso 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu akuti: “Taonani! Chihema cha Mulungu chili pakati pa anthu ndipo iye azidzakhala nawo. Iwo adzakhala anthu ake ndipo Mulunguyo adzakhala nawo.+
18 Chifukwa Yehova,Mlengi wakumwamba,+ Mulungu woona,Amene anaumba dziko lapansi, amene analipanga ndi kulikhazikitsa mwamphamvu,+Amene sanalilenge popanda cholinga,* koma analiumba kuti anthu akhalemo,+ wanena kuti: “Ine ndine Yehova ndipo palibenso wina.
3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu akuti: “Taonani! Chihema cha Mulungu chili pakati pa anthu ndipo iye azidzakhala nawo. Iwo adzakhala anthu ake ndipo Mulunguyo adzakhala nawo.+