Salimo 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumandidziwitsa njira ya moyo.+ Ndikakhala nanu pafupi,* ndimasangalala kwambiri.+Kudzanja lanu lamanja kuli chimwemwe* mpaka kalekale.
11 Mumandidziwitsa njira ya moyo.+ Ndikakhala nanu pafupi,* ndimasangalala kwambiri.+Kudzanja lanu lamanja kuli chimwemwe* mpaka kalekale.