Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+
11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+