Salimo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu ambiri akunena za ine* kuti: “Mulungu samupulumutsa ameneyu.”+ (Selah)* Salimo 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Misozi yanga ili ngati chakudya changa masana ndi usiku.Anthu amandinyoza tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+ Salimo 79:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+ Anthu a mitundu ina adziwe ife tikuonaKuti mwabwezera magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa.+
3 Misozi yanga ili ngati chakudya changa masana ndi usiku.Anthu amandinyoza tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+
10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+ Anthu a mitundu ina adziwe ife tikuonaKuti mwabwezera magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa.+