2 Samueli 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Davide ndi anthu onse a nyumba ya Isiraeli ankasangalala pamaso pa Yehova, akuimba mitundu yonse ya zoimbira za mtengo wofanana ndi mtengo wa mkungudza. Ankaimbanso zeze, zoimbira za zingwe,+ zinganga+ ndi maseche+ osiyanasiyana.
5 Davide ndi anthu onse a nyumba ya Isiraeli ankasangalala pamaso pa Yehova, akuimba mitundu yonse ya zoimbira za mtengo wofanana ndi mtengo wa mkungudza. Ankaimbanso zeze, zoimbira za zingwe,+ zinganga+ ndi maseche+ osiyanasiyana.