-
Yesaya 63:11-13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Iwo anakumbukira masiku akale,
Masiku a Mose mtumiki wake,
Ndipo anafunsa kuti: “Kodi amene anawatulutsa mʼnyanja+ pamodzi ndi abusa a anthu ake+ uja ali kuti?
Ali kuti amene anaika mzimu wake woyera mwa iye?+
12 Ali kuti amene anachititsa mkono wake waulemerero kuti upite ndi dzanja lamanja la Mose,+
Amene anagawanitsa madzi pamaso pawo+
Kuti adzipangire dzina lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+
13 Amene anawachititsa kuti adutse pamadzi amphamvu*
Moti anayenda osapunthwa,
Mofanana ndi hatchi mʼchipululu?*
-