-
Yesaya 11:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Adzaweruza mwachilungamo anthu onyozeka,
Ndipo adzadzudzula anthu mowongoka mtima, pothandiza ofatsa apadziko lapansi.
-
-
Aheberi 1:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndi mpando wako wachifumu+ mpaka kalekale ndipo ndodo ya Ufumu wako, ndi ndodo yachilungamo. 9 Unkakonda chilungamo ndipo unkadana ndi kusamvera malamulo. Nʼchifukwa chake Mulungu, Mulungu wako, anakudzoza+ ndi mafuta achisangalalo chachikulu kuposa mafumu anzako.”+
-