34 Koma ine ndikukuuzani kuti: Musamalumbire nʼkomwe,+ kutchula kumwamba, chifukwa nʼkumene kuli mpando wachifumu wa Mulungu, 35 kapena kutchula dziko lapansi chifukwa ndi chopondapo mapazi ake,+ kapenanso kutchula Yerusalemu chifukwa ndi mzinda wa Mfumu yamphamvu.+