1 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+ Salimo 104:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 104 Moyo wanga utamande Yehova.+ Inu Yehova Mulungu wanga, ndinu wamkulu kwambiri.+ Mwavala ulemu ndi ulemerero.+ Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu komanso zolengedwa zina zonse, atamande dzina la Yehova,Chifukwa dzina lake lokhalo lili pamwamba poti aliyense sangafikepo.+ Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+
27 Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+
104 Moyo wanga utamande Yehova.+ Inu Yehova Mulungu wanga, ndinu wamkulu kwambiri.+ Mwavala ulemu ndi ulemerero.+
13 Anthu komanso zolengedwa zina zonse, atamande dzina la Yehova,Chifukwa dzina lake lokhalo lili pamwamba poti aliyense sangafikepo.+ Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+