-
Luka 10:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pa nthawi imeneyo Yesu anasangalala kwambiri mwa mzimu woyera nʼkunena kuti: “Ndikukutamandani inu Atate pamaso pa onse, Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa anthu anzeru ndi ozindikira mwawabisira mosamala zinthu zimenezi+ ndipo mwaziulula kwa ana aangʼono. Inde Atate, chifukwa inu munavomereza kuti zimenezi zichitike.+
-