Salimo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu oipa adzapita ku Manda,*Anthu a mitundu yonse amene aiwala Mulungu adzapita kumeneko. Yeremiya 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi namwali angaiwale zinthu zake zodzikongoletsera?Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wapachifuwa?* Komatu anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+ Hoseya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu anga adzakhalitsidwa chete* chifukwa cha kusadziwa. Popeza iwo akana kundidziwa,+Inenso ndidzawakana kuti asamanditumikire ngati wansembe wanga.Komanso chifukwa chakuti iwo aiwala lamulo* la ine Mulungu wawo,+Inenso ndidzaiwala ana awo.
32 Kodi namwali angaiwale zinthu zake zodzikongoletsera?Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wapachifuwa?* Komatu anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+
6 Anthu anga adzakhalitsidwa chete* chifukwa cha kusadziwa. Popeza iwo akana kundidziwa,+Inenso ndidzawakana kuti asamanditumikire ngati wansembe wanga.Komanso chifukwa chakuti iwo aiwala lamulo* la ine Mulungu wawo,+Inenso ndidzaiwala ana awo.