Yobu 42:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova anadalitsa kwambiri mapeto a Yobu kuposa chiyambi chake+ moti iye anakhala ndi nkhosa 14,000, ngamila 6,000, ngʼombe 2,000* ndi abulu aakazi 1,000.+ 13 Anakhala ndi ana enanso aamuna 7 ndi ana aakazi atatu.+ Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+
12 Yehova anadalitsa kwambiri mapeto a Yobu kuposa chiyambi chake+ moti iye anakhala ndi nkhosa 14,000, ngamila 6,000, ngʼombe 2,000* ndi abulu aakazi 1,000.+ 13 Anakhala ndi ana enanso aamuna 7 ndi ana aakazi atatu.+
25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+