Danieli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu woona anachititsa kuti anyamata* 4 amenewa akhale odziwa zinthu komanso ozindikira zinthu zonse zolembedwa ndipo anawapatsa nzeru. Danieli anamupatsa nzeru zoti azitha kumvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+ Danieli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhani iliyonse yofunika nzeru komanso kuzindikira, imene mfumu inkawafunsa, inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake wonse.
17 Mulungu woona anachititsa kuti anyamata* 4 amenewa akhale odziwa zinthu komanso ozindikira zinthu zonse zolembedwa ndipo anawapatsa nzeru. Danieli anamupatsa nzeru zoti azitha kumvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+
20 Pa nkhani iliyonse yofunika nzeru komanso kuzindikira, imene mfumu inkawafunsa, inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake wonse.