Yobu 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+ Miyambo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuopa Yehova ndi chiyambi cha nzeru,+Ndipo ngati ungadziwe Mulungu, yemwe ndi Woyera Koposa,+ udzakhala womvetsa zinthu.
28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+
10 Kuopa Yehova ndi chiyambi cha nzeru,+Ndipo ngati ungadziwe Mulungu, yemwe ndi Woyera Koposa,+ udzakhala womvetsa zinthu.