-
1 Akorinto 13:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Panopa sitikuona bwinobwino chifukwa tikugwiritsa ntchito galasi losaoneka bwino, koma pa nthawiyo tizidzaona bwinobwino. Panopa sindikudziwa zonse, koma pa nthawiyo ndidzadziwa zonse ngati mmene Mulungu akundidziwira ineyo.
-