Miyambo 6:27-29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kodi munthu anganyamule makala a moto pachifuwa pake, zovala zake osapsa?+ 28 Kapena kodi munthu angayende pamakala a moto, mapazi ake osapsa? 29 Nʼchimodzimodzi ndi aliyense wogona ndi mkazi wa mnzake.Aliyense wokhudza mkaziyo adzalangidwa.+
27 Kodi munthu anganyamule makala a moto pachifuwa pake, zovala zake osapsa?+ 28 Kapena kodi munthu angayende pamakala a moto, mapazi ake osapsa? 29 Nʼchimodzimodzi ndi aliyense wogona ndi mkazi wa mnzake.Aliyense wokhudza mkaziyo adzalangidwa.+