1 Akorinto 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwamuna azipereka kwa mkazi wake zimene amafunikira,* mkazinso azipereka kwa mwamuna wake zimene amafunikira.+ Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posadetsedwa,+ chifukwa Mulungu adzaweruza achiwerewere* ndiponso achigololo.+
3 Mwamuna azipereka kwa mkazi wake zimene amafunikira,* mkazinso azipereka kwa mwamuna wake zimene amafunikira.+
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posadetsedwa,+ chifukwa Mulungu adzaweruza achiwerewere* ndiponso achigololo.+