2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maso a Yehova akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake* kwa anthu odzipereka ndi mtima wonse kwa iye.*+ Mwachita zopusa pa nkhani imeneyi. Kuyambira pano mʼdziko lanu muzichitika nkhondo.”+ Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali mʼkachisi wake wopatulika.+ Mpando wachifumu wa Yehova uli kumwamba.+ Maso ake amaona, inde maso ake* amayangʼanitsitsa ana a anthu.+ Salimo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwafufuza mtima wanga, mwandifufuza ngakhale usiku,+Ndipo mwandiyenga.+Mudzapeza kuti ndinalibe zolinga zochita choipa chilichonse.Ndipo pakamwa panga sipanachimwe. Yeremiya 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova ndimafufuza mtima,+Ndimafufuza maganizo a mkati mwa mtima wa munthu,*Kuti munthu aliyense ndimuchitire zinthu mogwirizana ndi zochita zake,Komanso mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+
9 Maso a Yehova akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake* kwa anthu odzipereka ndi mtima wonse kwa iye.*+ Mwachita zopusa pa nkhani imeneyi. Kuyambira pano mʼdziko lanu muzichitika nkhondo.”+
4 Yehova ali mʼkachisi wake wopatulika.+ Mpando wachifumu wa Yehova uli kumwamba.+ Maso ake amaona, inde maso ake* amayangʼanitsitsa ana a anthu.+
3 Mwafufuza mtima wanga, mwandifufuza ngakhale usiku,+Ndipo mwandiyenga.+Mudzapeza kuti ndinalibe zolinga zochita choipa chilichonse.Ndipo pakamwa panga sipanachimwe.
10 Ine Yehova ndimafufuza mtima,+Ndimafufuza maganizo a mkati mwa mtima wa munthu,*Kuti munthu aliyense ndimuchitire zinthu mogwirizana ndi zochita zake,Komanso mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+