14 Taonani munthu amene ali ndi pakati pa zinthu zoipa,
Watenga pakati pa mavuto ndipo adzabereka mabodza.+
15 Iye wakumba dzenje ndipo walizamitsa,
Koma adzagwera mʼdzenje limene wakumba yekhalo.+
16 Mavuto amene akuwayambitsawo adzabwerera pamutu pake,+
Zinthu zachiwawa zimene akuchita zidzagwera paliwombo pake.