Mateyu 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Uzithetsa nkhani mofulumira ndi munthu wokuimba mlandu pamene ukupita naye kukhoti, kuti mwina wokuimba mlanduyo asakakupereke kwa woweruza. Komanso kuti woweruzayo asakakupereke kwa msilikali wakukhoti kuti akuponye mʼndende.+
25 Uzithetsa nkhani mofulumira ndi munthu wokuimba mlandu pamene ukupita naye kukhoti, kuti mwina wokuimba mlanduyo asakakupereke kwa woweruza. Komanso kuti woweruzayo asakakupereke kwa msilikali wakukhoti kuti akuponye mʼndende.+