1 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso tisamachite chiwerewere,* mmene ena a iwo anachitira, nʼkufa anthu 23,000 tsiku limodzi.+