Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+ Salimo 101:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sindidzayangʼana chinthu chilichonse choipa.* Ndimadana ndi zochita za anthu amene asiya kuchita zinthu zabwino.+Sindidzalola kuti zochita zawozo zindikhudze. Miyambo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukhulupirika komanso chikondi chokhulupirika,+Ndipo chifukwa choopa Yehova, munthu amapewa kuchita zoipa.+ Aroma 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chikondi chanu chisakhale chachiphamaso.+ Muzinyansidwa ndi zoipa+ nʼkumayesetsa kuchita zabwino.
10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+
3 Sindidzayangʼana chinthu chilichonse choipa.* Ndimadana ndi zochita za anthu amene asiya kuchita zinthu zabwino.+Sindidzalola kuti zochita zawozo zindikhudze.
6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukhulupirika komanso chikondi chokhulupirika,+Ndipo chifukwa choopa Yehova, munthu amapewa kuchita zoipa.+