Yesaya 50:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wandipatsa lilime la anthu ophunzitsidwa bwino*+Kuti ndidziwe mmene ndingayankhire* munthu amene watopa, ndi mawu oyenera.+ Iye amandidzutsa mʼmawa uliwonse.Amandidzutsa kuti ndimvetsere* ngati mmene ophunzira amachitira.+
4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wandipatsa lilime la anthu ophunzitsidwa bwino*+Kuti ndidziwe mmene ndingayankhire* munthu amene watopa, ndi mawu oyenera.+ Iye amandidzutsa mʼmawa uliwonse.Amandidzutsa kuti ndimvetsere* ngati mmene ophunzira amachitira.+