-
Mateyu 7:24, 25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Choncho aliyense amene wamva mawu angawa nʼkuchita zimene wamvazo, adzafanana ndi munthu wanzeru, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+ 25 Ndiyeno kunagwa chimvula champhamvu ndipo madzi anasefukira. Kenako chimphepo chinawomba mwamphamvu, koma nyumbayo sinagwe chifukwa chakuti inakhazikika pathanthwepo.
-