Salimo 91:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+ Ndidzakhala naye pa nthawi ya mavuto.+ Ndidzamupulumutsa komanso kumupatsa ulemerero. 16 Ndidzamupatsa moyo wautali,+Ndipo ndidzamuchititsa kuti aone mmene ndidzamupulumutsire.”*+
15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+ Ndidzakhala naye pa nthawi ya mavuto.+ Ndidzamupulumutsa komanso kumupatsa ulemerero. 16 Ndidzamupatsa moyo wautali,+Ndipo ndidzamuchititsa kuti aone mmene ndidzamupulumutsire.”*+