Salimo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa anthu oipa adzaphedwa,+Koma amene akuyembekezera Yehova adzalandira dziko lapansi.+