Levitiko 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Muzikhala ndi masikelo olondola, miyala yolondola yoyezera kulemera kwa zinthu ndi miyezo yolondola.*+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo.
36 Muzikhala ndi masikelo olondola, miyala yolondola yoyezera kulemera kwa zinthu ndi miyezo yolondola.*+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo.