Machitidwe 20:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pa zinthu zonse ndakusonyezani kuti pogwira ntchito molimbikira chonchi,+ muzithandiza ofooka ndipo muzikumbukira mawu a Ambuye Yesu. Paja iye anati, ‘Kupatsa kumatichititsa kukhala osangalala kwambiri+ kuposa kulandira.’” 2 Akorinto 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nkhani imeneyi, wodzala moumira adzakolola zochepa ndipo wodzala mowolowa manja adzakolola zambiri.+
35 Pa zinthu zonse ndakusonyezani kuti pogwira ntchito molimbikira chonchi,+ muzithandiza ofooka ndipo muzikumbukira mawu a Ambuye Yesu. Paja iye anati, ‘Kupatsa kumatichititsa kukhala osangalala kwambiri+ kuposa kulandira.’”
6 Pa nkhani imeneyi, wodzala moumira adzakolola zochepa ndipo wodzala mowolowa manja adzakolola zambiri.+