Miyambo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mawu akachuluka sipalephera kukhala zolakwika,+Koma amene amalamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+ Mateyu 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu+ pa mawu aliwonse opanda pake amene iwo amalankhula.
19 Mawu akachuluka sipalephera kukhala zolakwika,+Koma amene amalamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+
36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu+ pa mawu aliwonse opanda pake amene iwo amalankhula.