Yesaya 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Makutu anu adzamva mawu kumbuyo kwanu akuti, “Njira ndi iyi.+ Yendani mʼnjira imeneyi,” kuti musasochere nʼkulowera kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
21 Makutu anu adzamva mawu kumbuyo kwanu akuti, “Njira ndi iyi.+ Yendani mʼnjira imeneyi,” kuti musasochere nʼkulowera kudzanja lamanja kapena lamanzere.+