Salimo 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zinthu zochepa zimene munthu wolungama ali nazo ndi zabwinoKusiyana ndi zinthu zochuluka za anthu ambiri oipa.+ Yeremiya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu amene amapeza chuma mwachinyengo,*+Ali ngati nkhwali imene imasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho chidzatha asanakwanitse hafu ya zaka za moyo wake,Ndipo pamapeto pake adzadziwika kuti ndi wopusa.”
16 Zinthu zochepa zimene munthu wolungama ali nazo ndi zabwinoKusiyana ndi zinthu zochuluka za anthu ambiri oipa.+
11 Munthu amene amapeza chuma mwachinyengo,*+Ali ngati nkhwali imene imasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho chidzatha asanakwanitse hafu ya zaka za moyo wake,Ndipo pamapeto pake adzadziwika kuti ndi wopusa.”