Yakobo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lilimenso ndi moto.+ Pa ziwalo zonse za thupi lathu, lilime ndi lodzaza ndi zinthu zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse+ komanso limayatsa moyo wonse wa munthu* ndipo lili ndi moto wa Gehena.*
6 Lilimenso ndi moto.+ Pa ziwalo zonse za thupi lathu, lilime ndi lodzaza ndi zinthu zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse+ komanso limayatsa moyo wonse wa munthu* ndipo lili ndi moto wa Gehena.*