Yakobo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa pamene pali nsanje ndi mtima wokonda mikangano,* pamakhalanso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+
16 Chifukwa pamene pali nsanje ndi mtima wokonda mikangano,* pamakhalanso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+