-
Genesis 13:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Choncho Abulamu anauza Loti+ kuti: “Chonde, pasakhale mkangano uliwonse pakati pa ine ndi iwe, komanso pakati pa abusa anga ndi abusa ako, pajatu ndife pachibale. 9 Tiye tisiyane. Ukhoza kusankha mbali iliyonse ya dzikoli. Iwe ukapita kumanzere, ine ndipita kumanja, koma ukapita kumanja, ine ndipita kumanzere.”
-