8 Koma anthu amantha, opanda chikhulupiriro,+ odetsedwa amenenso amachita zinthu zonyansa, opha anthu,+ achiwerewere,+ amene amachita zamizimu, olambira mafano ndi anthu onse abodza,+ adzaponyedwa mʼnyanja yoyaka moto ndi sulufule.+ Nyanja imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.”+