Mika 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino. Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani? Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+
8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino. Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani? Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+