-
1 Mafumu 21:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mʼmakalatawo analembamo kuti: “Uzani anthu kuti asale kudya ndipo Naboti mumuike kutsogolo kwa anthu onse. 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri opanda pake adzakhale kutsogolo kwake nʼkupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe wanyoza Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja nʼkumuponya miyala kuti afe.”+
-