Salimo 61:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzatalikitsa moyo wa mfumu,*+Ndipo idzakhala ndi moyo ku mibadwomibadwo. 7 Mfumuyo idzakhala pampando wachifumu mpaka kalekale pamaso pa Mulungu.+Chikondi chanu chokhulupirika komanso kukhulupirika kwanu ziiteteze.+
6 Mudzatalikitsa moyo wa mfumu,*+Ndipo idzakhala ndi moyo ku mibadwomibadwo. 7 Mfumuyo idzakhala pampando wachifumu mpaka kalekale pamaso pa Mulungu.+Chikondi chanu chokhulupirika komanso kukhulupirika kwanu ziiteteze.+