18 Oweruzawo azifufuza nkhaniyo mosamala+ ndipo ngati munthu amene anapereka umboniyo wapezeka kuti amanama ndipo waneneza mʼbale wake mlandu wabodza, 19 muzimuchitira zimene amafuna kuti zichitikire mʼbale wakezo,+ ndipo muzichotsa woipayo pakati panu.+