Miyambo 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amene sakwapula* mwana wake ndiye kuti akudana naye,+Koma amene amamukonda salephera* kumupatsa chilango.+ Miyambo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Langa mwana wako padakali chiyembekezo,+Ndipo usakhale ndi mlandu wochititsa* kuti afe.+ Aefeso 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu abambo, musamapsetse mtima ana anu,+ koma pitirizani kuwalera powapatsa malangizo*+ komanso kuwaphunzitsa mogwirizana ndi zimene Yehova* amanena.+
24 Munthu amene sakwapula* mwana wake ndiye kuti akudana naye,+Koma amene amamukonda salephera* kumupatsa chilango.+
4 Inu abambo, musamapsetse mtima ana anu,+ koma pitirizani kuwalera powapatsa malangizo*+ komanso kuwaphunzitsa mogwirizana ndi zimene Yehova* amanena.+