Salimo 111:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+ ש [Sin] Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+ ת [Taw] Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale. 2 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Okondedwa, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi ndi mzimu,+ kuti tikhale oyera pamene tikuopa Mulungu.
10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+ ש [Sin] Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+ ת [Taw] Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale.
7 Okondedwa, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi ndi mzimu,+ kuti tikhale oyera pamene tikuopa Mulungu.