Miyambo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Upeze nzeru, upezenso luso lomvetsa zinthu.+ Usaiwale ndipo usapatuke pa zimene ndimakuuza. Miyambo 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kupeza nzeru nʼkwabwino kwambiri kuposa kupeza golide.+ Ndipo ndi bwino kusankha kumvetsa zinthu kuposa siliva.+
16 Kupeza nzeru nʼkwabwino kwambiri kuposa kupeza golide.+ Ndipo ndi bwino kusankha kumvetsa zinthu kuposa siliva.+