Aroma 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma “ngati mdani wako ali ndi njala, umʼpatse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, umʼpatse chakumwa. Chifukwa ukatero udzamuunjikira makala a moto pamutu pake.”*+
20 Koma “ngati mdani wako ali ndi njala, umʼpatse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, umʼpatse chakumwa. Chifukwa ukatero udzamuunjikira makala a moto pamutu pake.”*+