-
Yobu 1:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu? Padziko lapansi palibe wina wofanana naye. Iye ndi munthu wokhulupirika amene amachita zoyenera,*+ amaopa Mulungu ndiponso amapewa zoipa.” 9 Ndiyeno Satana anayankha Yehova kuti: “Kodi mukuganiza kuti Yobu amangoopa Mulungu popanda chifukwa?+
-